Yohane 6:60-62 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

60. 14 Pamenepo ambiri a akuphunzira ace, pakumva izi, anati, Mau awa ndi osautsa; akhoza kumva awa ndani?

61. Koma Yesu podziwa mwa yekha kuti akuphunzira ace alikung'ung'udza cifukwa ca ici, anati kwa iwo, ici mukhumudwa naco?

62. 15 Nanga bwanji ngati mukaona Mwana wa munthu alikukwera kumene anali kale lomwe?

Yohane 6