Yohane 6:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kulibe mmodzi akhoza kudza kwa Ine koma ngati Atate wondituma Ine amkoka iye; ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomariza.

Yohane 6

Yohane 6:42-46