Yohane 6:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo ananena, Si Yesu uyu, mwana wa Yosefe, atate wace ndi amai wace tiwadziwa? Anena bwanji tsopano, kuti, Ndinatsika Kumwamba?

Yohane 6

Yohane 6:39-48