Yohane 5:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca ici Ayuda anaonjeza kufuna kumupha, si cifukwa ca kuswa dzuwa la Sabata kokha, komatu amaehanso Mulungu Atate wace wa iye yekha; nadziyesera wolingana ndi Mulungu.

Yohane 5

Yohane 5:17-28