Yohane 3:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yohane analinkubatiza m'Ainoni pafupi pa Salemu, cifukwa panali madzi ambiri pamenepo; ndipo analinkufikako anthu, nalinkubatizidwa.

Yohane 3

Yohane 3:21-30