Yohane 19:41-42 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Koma kunali munda kumalo kumene anapacikidwako, ndi m'mundamo munali manda atsopano m'mene sanaikidwamo munthu ali