Yohane 19:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu anamyankha iye, Simukadakhala nao ulamuliro uli wonse pa Ine, ngati sukadapatsidwa kwa inu kucokera Kumwamba; cifukwa ca ici iye wondipereka Ine kwa inu ali nalo cimo loposa.

Yohane 19

Yohane 19:5-14