Yohane 15:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukadakhala a dziko lapansi, dziko lapansi likadakonda zace za lokha; koma popeza simuli a dziko lapansi, koma Ine ndinakusankhani inu mwa dziko lapansi, cifukwa ca ici likudani inu.

Yohane 15

Yohane 15:15-24