Yohane 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mtima wanu usabvutike; mukhulupirira Mulungu, khulupirirani Inenso.

2. M'nyumba ya Atate wanga alimo malo okhalamo ambiri. Ngati sikudali kutero, ndikadakuuzani inu; pakuti ndipita kukukonzerani inu malo.

Yohane 14