Yohane 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Petro ananena ndi iye, Simudzasambitsa mapazi anga ku nthawi yonse. Yesu anamyankha iye, Ngati sindikusambitsa iwe ulibe colandira pamodzi ndi Ine.

Yohane 13

Yohane 13:1-10