Yohane 12:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti mau a Yesaya mneneri akakwaniridwe, amene anati,3 Ambuye, wakhulupirira ndani kulalikira kwathu?Ndipo mkono wa Ambuye wabvumbulutsidwa kwa yani?

Yohane 12

Yohane 12:28-42