Yohane 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akuphunzira ananena ndi iye, Ambuye, Ayuda analikufuna kukuponyani miyala tsopano apa; ndipo munkanso komweko kodi?

Yohane 11

Yohane 11:6-13