Yobu 42:16-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo zitatha izi, Yobu anakhala ndi moyo zaka zana limodzi mphambu makumi anai, naona ana ace ndi zidzukulu zace