Yobu 42:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Anali naonso ana amuna asanu ndi awiri ndi ana akazi atatu.

14. Ndipo anamucha dzina la woyamba Yemima, ndi dzina la waciwiri Keziya, ndi dzina la wacitatu Kerenihapuki.

15. Ndipo m'dziko monse simunapezeka akazi okongola ngati ana akazi a Yobu, nawapatsa colowa atate wao pamodzi ndi alongo ao.

Yobu 42