Yobu 39:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Kodi ciombankhanga cikwera m'mwamba pocilamulira iwe,Nicimanga cisanja cace m'mwamba?

28. Kwao nku thanthwe, cigona komweko,Pansonga pa thanthwe pokhazikikapo.

29. Pokhala kumeneko ciyang'ana cakudya;Maso ace acipenyetsetsa ciri kutali,

Yobu 39