Yobu 38:19-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Iri kuti njira yomukira pokhala kuunika?Ndi mdima, pokhala pace pali kuti,

20. Kuti upite nao ku malire ace,Kuti uzindikire miseu ya ku nyumba yace?

21. Udziwa, pakuti unabadwa pamenepo,Ndi masiku ako acuruka kuwerenga kwao.

22. Kodi unalowa m'zosungiramo cipale cofewa?Kapena unapenya zosungiramo matalala,

Yobu 38