Yobu 36:31-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pakuti aweruza nazo mitundu ya anthu.Apatsa cakudya cocuruka. Akutidwa manja ace ndi mphezi,Nailamulira igwere