Yobu 34:24-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Aphwanya eni mphamvu osaturutsa kubwalo mlandu wao,Naika ena m'malo mwao.

25. Pakuti asamalira nchito zao,Nawagubuduza usiku kuti aphwanyike.

26. Awakantha ngati oipa,Poyera pamaso pa anthu.

27. Popeza anapambuka, naleka kumtsata,Osasamalira njira zace ziri zonse.

Yobu 34