Yobu 34:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga kwa Iye wosasamalira nkhope za akalonga,Wosasiyanitsa pakati pa wolemera ndi wosauka?Pakuti onsewo ndiwo nchito ya manja ace.

Yobu 34

Yobu 34:13-21