Yobu 34:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Elihu anabwereza kunena, nati,

2. Tamverani mau anga, inu anzeru;Mundicherere khutu inu akudziwa.

3. Pakuti khutu liyesa mau,Monga m'kamwa mulawa cakudya.

Yobu 34