Yobu 31:36-39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

36. Ndithu ndikadawasenza paphewa panga,Ndi kudzimangirira awa ngati korona.

37. Ndikadamfotokozera ciwerengo ca mopondamo mwanga,Ndikadamsenderera Iye ngati ka longa,

38. Ngati minda yanga ipfuula monditsutsa,Ndi nthumbira zace zilira pamodzi;

39. Ngati ndadya zipatso zace wopanda ndarama,Kapena kutayitsa eni ace moyo wao;

Yobu 31