Yobu 31:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Si ndizo cionongeko ca wosalungama,Ndi tsoka la ocita mphulupulu?

4. Nanga sapenyanjira zanga,Ndi kuwerenga moponda mwanga monse?

5. Ngati ndinayanjana nalo bodza,Ndi phazi langa linathamangira cinyengo;

Yobu 31