Yobu 3:25-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Pakuti cimene ndinaciopa candigwera,Ndi cimene ndacita naco mantha candidzera.

26. Wosakhazikika, ndi wosakhala cete, ndi wosapumula ine,Koma mabvuto anandidzera.

Yobu 3