Yobu 27:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Zoopsa zimgwera ngati madzi;Nkuntho umtenga usiku.

21. Mphepo ya kum'mawa Imtenga, nacokaiye;Nimkankha acoke m'malo mwace.

22. Pakuti Mulungu adzamponyera zoopsa, osanlieka;Kuthawa akadathawa m'dzanja lace.

Yobu 27