Yobu 24:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Awalola akhale osatekeseka, ndipo alimbikapo;Koma maso ace ali pa njira zao.

24. Akwezeka; m'kamphindi kuti zi;Inde atsitsidwa, acotsedwa monga onse ena,Adutidwa ngati tirigu ngala zace.

25. Ndipo ngati si kutero, anditsutsa ndani kuti ndiri wabodza,Ndi kuyesa mau anga opanda pace?

Yobu 24