Yobu 24:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Wamphamvuyonse alekeranji kuikiratu nyengo?Ndi iwo omdziwa alekeranji kudziwa masiku ace?

2. Alipo akusendeza malire;Alanda gulu la zoweta, nazidyetsa.

3. Akankhizira kwao buru wa amasiye,Atenga ng'ombe ya mfedwa ikhale cikole.

4. Apambukitsa aumphawi m'njira;Osauka a padziko abisala pamodzi.

Yobu 24