Yobu 20:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Phindu la m'nyumba mwace lidzacoka,Akatundu ace adzamthawa tsiku la mkwiyo wace. Ili ndi gawo la munthu woipa