Yobu 18:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Akudza m'mbuyo adzadabwa nalo tsiku lace,Monga aja omtsogolera anagwidwa mantha.

21. Zoonadi, zokhalamo osalungama zitero,Ndi malo a iye amene sadziwa Mulungu ndi awa.

Yobu 18