Yobu 18:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati,

2. Musaka mau kufikira liti?Zindikirani, ndi pamenepo tidzanena.

3. Tiyesedwa bwanji ngati nyama za kuthengo,Ndi kukhala odetsedwa pamaso panu?

Yobu 18