Yobu 15:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Pakuti pakamwa pako paphunzitsa mphulupulu zako,Nusankha lilime la ocenjerera.

6. Pakamwa pako pakutsutsa, si ine ai.Inde milomo yako ikucitira umboni wakukutsutsa.

7. Kodi ndiwe munthu woyamba kubadwa?Kapena unayamba kulengedwa ndiwe, osati mapiri?

Yobu 15