Yobu 15:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati,

2. Kodi mwini nzeru ayankhe ndi kudziwa kouluzika,Ndi kudzaza mimba yace ndi mphepo ya kum'mawa?

3. Kodi atsutsane ndi mnzace ndi mau akusathandiza?Kapena ndi maneno akusaphindulitsa?

Yobu 15