Yobu 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Munthu wobadwa ndi mkaziNgwa masiku owerengeka, nakhuta mabvuto,

2. Aturuka ngati duwa, nafota;Athawa ngati mthunzi, osakhalitsa.

Yobu 14