Yobu 13:27-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Mulonganso mapazi anga m'zigologolo, ndi kupenyerera mayendedwe anga onse;Mudzilembera malire mopanika mapazi anga;

28. Momwemo munthu akutha ngati cinthu coola,Ngati cobvala codyedwa ndi numbi

Yobu 13