Yobu 11:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo anayankha Zofari wa ku Naama, nati,

2. Kodi mau ocurukawa sayenera kuwayankha?Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?

Yobu 11