Yesaya 66:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo adzaturuka ndi kuyang'ana mitembo ya anthu amene andilakwira Ine, pakuti mbozi yao sidzafa, pena moto wao sudzazimidwa; ndipo iwo adzanyansa anthu onse.

Yesaya 66

Yesaya 66:20-24