Yesaya 66:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sangalalani inu pamodzi ndi Yerusalemu, ndipo kondwani cifukwa ca iye, inu nonse amene mumkonda; sangalalani kokondwa pamodzi ndi iye, inu nonse akumlira maliro;

Yesaya 66

Yesaya 66:1-13