Yesaya 65:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo sadzagwira nchito mwacabe, pena kubalira tsoka; pakuti iwo ndiwo mbeu ya odalitsidwa a Yehova, ndi obadwa ao adzakhala pamodzi ndi iwo.

Yesaya 65

Yesaya 65:21-25