Yesaya 65:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzasiya dzina lanu likhale citemberero kwa osankhidwa anga, ndipo Ambuye Yehova adzakupha iwe, nadzacha atumiki ace dzina lina;

Yesaya 65

Yesaya 65:14-24