Yesaya 61:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo adzamanga mabwinja akale, nadzamanga pa miunda yakale, nadzakonzanso midzi yopasuka, mabwinja a mibadwo yambiri.

Yesaya 61

Yesaya 61:1-9