Yesaya 58:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo amene adzakhala a iwe adzamanga malo akale abwinja; udzautsa maziko a mibadwo yambiri; udzachedwa Wokonza pogumuka, Wakubwezera njira zakukhalamo.

Yesaya 58

Yesaya 58:11-14