Yesaya 57:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndi yani amene wamuopa ndi kucita naye mantha, kuti wanama, osandikumbukira Ine, kapena kundisamalira? Kodi Ine sindinakhala cete nthawi yambiri, ndipo iwe sunandiopa Ine konse?

Yesaya 57

Yesaya 57:6-20