Yesaya 55:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti monga kumwamba kuli kutari ndi dziko lapansi, momwemo njira zanga ziri zazitari kupambana njira zanu, ndi maganizo anga kupambana maganizo anu.

Yesaya 55

Yesaya 55:3-13