Yesaya 55:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu nonse, inu akumva ludzu, idzani kumadzi; ndi osowa ndarama idzani inu mugule mudye; inde idzani, mugule vinyo ndi mkaka opanda ndarama ndi opanda mtengo wace.

Yesaya 55

Yesaya 55:1-4