Yesaya 5:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ana a nkhosa adzadyapo ngati m'busa mwao, ndi malo a bwinja a zonenepa zacilendo zidzadyapo.

Yesaya 5

Yesaya 5:9-18