Yesaya 48:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo sanamva ludzu, pamene Iye anawatsogolera m'mapululu; anawaturutsira madzi kuturuka m'matanthwe; anadulanso thanthwe, madzi nabulika.

Yesaya 48

Yesaya 48:12-22