Yesaya 44:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma tsopano, imva Yakobo, mtumiki wanga, ndi Israyeli, amene ndakusankha;

2. atero Yehova, amene anakutenga iwe, nakuumba kucokera m'mimba, amene adzathangata iwe. Usaope Yakobo, mtumiki wanga ndi iwe, Yesuruni, amene ndakusankha iwe.

Yesaya 44