Yesaya 39:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana ako amene adzabadwa ndi iwe, amene udzabala, iwo adzawatenga, ndipo adzakhala adindo m'cinyumba cace ca mfumu ya ku Babulo.

Yesaya 39

Yesaya 39:1-8