Yesaya 35:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiro oomboledwa a Yehova adzabwera, nadzafika ku Ziyoni alikuyimba; kukondwa kosatha kudzakhala pa mitu yao; iwo adzakhala ndi kusekerera ndi kukondwa, ndipo cisoni ndi kuusa moyo kudzacoka.

Yesaya 35

Yesaya 35:1-10