Yesaya 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Maonekedwe a nkhope zao awacitira iwo mboni; ndipo amaonetsa ucimo wao monga Sodomu, saubisa. Tsoka kwa moyo wao! cifukwa iwo anadzicitira zoipa iwo okha.

Yesaya 3

Yesaya 3:3-13