Yesaya 26:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tsiku limenelo adzayimba nyimbo imeneyi m'dziko la Yuda, Ife tiri ndi mudzi wolimba; Iye adzaikacipulumutso cikhale macemba ndi malinga.

2. Tsegulani pazipata, kuti mtundu wolungama, umene ucita zoonadi, ulowemo.

3. Inu mudzasunga mtima wokhazikika mu mtendere weni weni, cifukwa ukukhulupirirani Inu.

Yesaya 26